Oweruza 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Panali mitengo imene inkafuna kudzoza mfumu yawo. Choncho inauza mtengo wa maolivi kuti, ‘Ukhale mfumu yathu.’+
8 Panali mitengo imene inkafuna kudzoza mfumu yawo. Choncho inauza mtengo wa maolivi kuti, ‘Ukhale mfumu yathu.’+