Oweruza 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ngati si choncho, moto utuluke mwa Abimeleki nʼkuwotcha atsogoleri a ku Sekemu ndi ku Beti-milo,+ komanso moto utuluke mwa atsogoleri a ku Sekemu ndi ku Beti-milo nʼkuwotcha Abimeleki.”+
20 Koma ngati si choncho, moto utuluke mwa Abimeleki nʼkuwotcha atsogoleri a ku Sekemu ndi ku Beti-milo,+ komanso moto utuluke mwa atsogoleri a ku Sekemu ndi ku Beti-milo nʼkuwotcha Abimeleki.”+