Oweruza 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwo anapita mʼmunda nʼkukathyola mphesa, kuziponda ndipo kenako anachita chikondwerero. Atatero analowa mʼnyumba ya mulungu wawo+ nʼkuyamba kudya, kumwa ndi kutemberera Abimeleki.
27 Iwo anapita mʼmunda nʼkukathyola mphesa, kuziponda ndipo kenako anachita chikondwerero. Atatero analowa mʼnyumba ya mulungu wawo+ nʼkuyamba kudya, kumwa ndi kutemberera Abimeleki.