-
Oweruza 9:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Ndiyeno mawa dzuwa likangotuluka, mudzadzuke nʼkuukira mzindawu. Ndipo iye ndi anthu amene ali nawo akadzatuluka kudzamenyana nanu, mudzachite chilichonse chomwe mungathe kuti mumʼgonjetse.”
-