-
Oweruza 9:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Atamva zimenezi anatenga anthu ake nʼkuwagawa mʼmagulu atatu ndipo anabisalira anthuwo mʼtchire. Ataona anthu akutuluka mumzindawo, anapita nʼkukawapha.
-