Oweruza 9:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndiyeno Abimeleki anamenyana ndi anthu amumzindawo tsiku lonse nʼkuulanda. Anapha anthu amene anali mumzindawo ndipo anaugwetsa+ nʼkuthira mchere panthaka ya mzindawo.
45 Ndiyeno Abimeleki anamenyana ndi anthu amumzindawo tsiku lonse nʼkuulanda. Anapha anthu amene anali mumzindawo ndipo anaugwetsa+ nʼkuthira mchere panthaka ya mzindawo.