-
Oweruza 9:49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 Ndiyeno aliyense anadula nthambi yake nʼkutsatira Abimeleki. Kenako anaika nthambizo pachipinda chotetezekacho nʼkuchiyatsa moto. Choncho anthu onse okhala munsanja ya Sekemu, amuna ndi akazi pafupifupi 1,000, anafa.
-