Oweruza 9:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Zitatero, mayi wina anaponya mwala wa mphero pamutu wa Abimeleki nʼkuuphwanya.+