-
Oweruza 9:54Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
54 Nthawi yomweyo, Abimeleki anaitana mtumiki wake womunyamulira zida nʼkumuuza kuti: “Tenga lupanga lako undiphe, kuti anthu asadzanene kuti, ‘Anaphedwa ndi mkazi.’” Atatero, mtumiki wakeyo anamubaya ndi lupanga, ndipo anafa.
-