Oweruza 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anali ndi ana 30 aamuna amene ankayenda pa abulu 30, ndipo iwo anali ndi mizinda 30. Mpaka lero mizinda imeneyi imadziwikabe kuti Havoti-yairi+ ndipo ili ku Giliyadi.
4 Iye anali ndi ana 30 aamuna amene ankayenda pa abulu 30, ndipo iwo anali ndi mizinda 30. Mpaka lero mizinda imeneyi imadziwikabe kuti Havoti-yairi+ ndipo ili ku Giliyadi.