Oweruza 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zitatero, Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli moti anawapereka* kwa Afilisiti ndi kwa Aamoni.+