-
Oweruza 10:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Choncho, anthu amenewa anazunza ndi kupondereza kwambiri Aisiraeli chaka chimenecho. Kwa zaka 18, anapondereza Aisiraeli onse amene anali kumʼmawa kwa Yorodano, mʼdziko la Aamori limene linali ku Giliyadi.
-