Oweruza 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zitatero Aisiraeli anapempha Yehova kuti awathandize.+ Iwo anati: “Takuchimwirani inu Mulungu wathu, chifukwa tinakusiyani nʼkuyamba kutumikira Abaala.”+
10 Zitatero Aisiraeli anapempha Yehova kuti awathandize.+ Iwo anati: “Takuchimwirani inu Mulungu wathu, chifukwa tinakusiyani nʼkuyamba kutumikira Abaala.”+