-
Oweruza 10:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Koma Aisiraeli anauza Yehova kuti: “Tachimwa. Inuyo mutichite chilichonse chimene mukuona kuti nʼchabwino. Koma panopa chonde tipulumutseni.”
-