Oweruza 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atatero, iwo anachotsa milungu yonse yachilendo imene anali nayo ndipo anayamba kutumikira Yehova,+ moti iye sanalole kuti Aisiraeli apitirize kuvutika.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:16 Yandikirani, ptsa. 254-255, 259
16 Atatero, iwo anachotsa milungu yonse yachilendo imene anali nayo ndipo anayamba kutumikira Yehova,+ moti iye sanalole kuti Aisiraeli apitirize kuvutika.+