-
Oweruza 11:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho Yefita anathawa azichimwene akewo ndipo anakakhala ku Tobu. Kumeneko anthu osowa zochita anagwirizana ndi Yefita ndipo ankapita naye limodzi kukaukira adani awo.
-