-
Oweruza 11:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno Yefita anauza akulu a ku Giliyadiwo kuti: “Ngati mukunditenga kuti tikamenyane ndi Aamoni, ndipo Yehova nʼkukandithandiza kuwagonjetsa, ndidzakhaladi mtsogoleri wanu.”
-