Oweruza 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Yefita anapita ndi akulu a ku Giliyadi, ndipo anthu anamuika kukhala mtsogoleri wawo komanso mkulu wa asilikali. Ndiyeno Yefita anabwerezanso kunena mawu ake onse aja pamaso pa Yehova ku Mizipa.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:11 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2016, ptsa. 6-7
11 Choncho Yefita anapita ndi akulu a ku Giliyadi, ndipo anthu anamuika kukhala mtsogoleri wawo komanso mkulu wa asilikali. Ndiyeno Yefita anabwerezanso kunena mawu ake onse aja pamaso pa Yehova ku Mizipa.+