Oweruza 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene ankadutsa mʼchipululu, analambalala dziko la Edomu+ ndi la Mowabu. Anadutsa chakumʼmawa kwa dziko la Mowabu+ nʼkukamanga misasa mʼchigawo cha Arinoni. Iwo sanadutse malire a Mowabu chifukwa Arinoni ndi amene anali malire a Mowabu.+
18 Pamene ankadutsa mʼchipululu, analambalala dziko la Edomu+ ndi la Mowabu. Anadutsa chakumʼmawa kwa dziko la Mowabu+ nʼkukamanga misasa mʼchigawo cha Arinoni. Iwo sanadutse malire a Mowabu chifukwa Arinoni ndi amene anali malire a Mowabu.+