Oweruza 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Aisiraeli anatumiza uthenga kwa Sihoni mfumu ya Aamori, ya ku Hesiboni, kuti: “Tingadutse nawo mʼdziko lanu kupita kumalo athu?”+
19 Kenako Aisiraeli anatumiza uthenga kwa Sihoni mfumu ya Aamori, ya ku Hesiboni, kuti: “Tingadutse nawo mʼdziko lanu kupita kumalo athu?”+