Oweruza 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Sihoni sanakhulupirire kuti Aisiraeli akufuna kungodutsa mʼdziko lake. Choncho Sihoni anasonkhanitsa anthu ake onse nʼkumanga misasa ku Yahazi ndipo anayamba kumenyana ndi Aisiraeliwo.+
20 Koma Sihoni sanakhulupirire kuti Aisiraeli akufuna kungodutsa mʼdziko lake. Choncho Sihoni anasonkhanitsa anthu ake onse nʼkumanga misasa ku Yahazi ndipo anayamba kumenyana ndi Aisiraeliwo.+