Oweruza 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zitatero, Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka Sihoni ndi anthu ake onse mʼmanja mwa Aisiraeli. Choncho anawagonjetsa nʼkutenga dziko lonse la Aamori okhala kumeneko.+
21 Zitatero, Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka Sihoni ndi anthu ake onse mʼmanja mwa Aisiraeli. Choncho anawagonjetsa nʼkutenga dziko lonse la Aamori okhala kumeneko.+