Oweruza 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiye iweyo wasiyana pati ndi Balaki+ mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu? Kodi iye anakwanitsa kulimbana ndi Aisiraeli, kapena anayesa nʼkomwe kumenyana nawo?
25 Ndiye iweyo wasiyana pati ndi Balaki+ mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu? Kodi iye anakwanitsa kulimbana ndi Aisiraeli, kapena anayesa nʼkomwe kumenyana nawo?