Oweruza 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamene Aisiraeli ankakhala ku Hesiboni ndi mʼmidzi yake yozungulira,+ ku Aroweli ndi mʼmidzi yake yozungulira ndi mʼmizinda yonse yamʼmbali mwa nyanja ku Arinoni kwa zaka 300, nʼchifukwa chiyani simunawalande mizindayo pa nthawi imeneyo?+
26 Pamene Aisiraeli ankakhala ku Hesiboni ndi mʼmidzi yake yozungulira,+ ku Aroweli ndi mʼmidzi yake yozungulira ndi mʼmizinda yonse yamʼmbali mwa nyanja ku Arinoni kwa zaka 300, nʼchifukwa chiyani simunawalande mizindayo pa nthawi imeneyo?+