Oweruza 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mzimu wa Yehova unapatsa mphamvu Yefita+ ndipo anadutsa mʼdera la Giliyadi ndi la Manase nʼkukafika mʼdera la Mizipe wa ku Giliyadi.+ Atafika mʼdera la Mizipe wa ku Giliyadi anapitirira mpaka kukafika kwa Aamoni. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:29 Nsanja ya Olonda,5/15/2007, tsa. 9
29 Mzimu wa Yehova unapatsa mphamvu Yefita+ ndipo anadutsa mʼdera la Giliyadi ndi la Manase nʼkukafika mʼdera la Mizipe wa ku Giliyadi.+ Atafika mʼdera la Mizipe wa ku Giliyadi anapitirira mpaka kukafika kwa Aamoni.