Oweruza 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atangomuona, anangʼamba zovala zake nʼkunena kuti: “Mayine mwana wanga! Ndikumva chisoni kwambiri chifukwa ndikukuchotsa pakhomo. Ndalonjeza kwa Yehova ndipo sindingathe kubweza mawu anga.”+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:35 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2017, tsa. 4 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2016, ptsa. 7-8
35 Atangomuona, anangʼamba zovala zake nʼkunena kuti: “Mayine mwana wanga! Ndikumva chisoni kwambiri chifukwa ndikukuchotsa pakhomo. Ndalonjeza kwa Yehova ndipo sindingathe kubweza mawu anga.”+