Oweruza 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma iye anati: “Bambo, ngati mwalonjeza kwa Yehova, ndichitireni mogwirizana ndi zimene mwanenazo,+ chifukwa Yehova wakumenyerani nkhondo pobwezera adani anu, Aamoni.” Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:36 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2016, ptsa. 8-9 Nsanja ya Olonda,5/15/2007, tsa. 10
36 Koma iye anati: “Bambo, ngati mwalonjeza kwa Yehova, ndichitireni mogwirizana ndi zimene mwanenazo,+ chifukwa Yehova wakumenyerani nkhondo pobwezera adani anu, Aamoni.”