Oweruza 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno amuna a ku Efuraimu anasonkhana pamodzi nʼkuwoloka kupita ku Zafoni,* ndipo anauza Yefita kuti: “Nʼchifukwa chiyani unapita kukamenyana ndi Aamoni osatiitana kuti tipite limodzi?+ Tiwotcha nyumba yako iwe uli momwemo.”
12 Ndiyeno amuna a ku Efuraimu anasonkhana pamodzi nʼkuwoloka kupita ku Zafoni,* ndipo anauza Yefita kuti: “Nʼchifukwa chiyani unapita kukamenyana ndi Aamoni osatiitana kuti tipite limodzi?+ Tiwotcha nyumba yako iwe uli momwemo.”