Oweruza 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno tsiku lina, mngelo wa Yehova anaonekera kwa mkaziyo nʼkumuuza kuti: “Tamvera, ndiwe wosabereka ndipo ulibe mwana. Koma udzakhala ndi pakati ndipo udzabereka mwana wamwamuna.+
3 Ndiyeno tsiku lina, mngelo wa Yehova anaonekera kwa mkaziyo nʼkumuuza kuti: “Tamvera, ndiwe wosabereka ndipo ulibe mwana. Koma udzakhala ndi pakati ndipo udzabereka mwana wamwamuna.+