Oweruza 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Udzakhala ndi pakati ndipo udzabereka mwana wamwamuna. Mʼmutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri* wa Mulungu kuchokera tsiku limene adzabadwe.* Iye adzatsogolera populumutsa Isiraeli mʼmanja mwa Afilisiti.”+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2152 Nsanja ya Olonda,3/15/2005, tsa. 25
5 Udzakhala ndi pakati ndipo udzabereka mwana wamwamuna. Mʼmutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri* wa Mulungu kuchokera tsiku limene adzabadwe.* Iye adzatsogolera populumutsa Isiraeli mʼmanja mwa Afilisiti.”+