-
Oweruza 13:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Manowa anachonderera Yehova kuti: “Yehova, tikupempha kuti munthu wa Mulungu woona amene munamutuma uja, abwerenso kuti adzatilangize zoyenera kuchita ndi mwana amene adzabadweyo.”
-