-
Oweruza 13:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma mngelo wa Yehova anauza Manowa kuti: “Ngakhale nditati ndidikire sikuti ndidya chakudya chanu. Koma ngati mungakonde kupereka kwa Yehova nsembe yopsereza, perekani.” Manowa sanadziwe kuti anali mngelo wa Yehova.
-