Oweruza 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma mkazi wakeyo anati: “Yehova akanakhala kuti akufuna kutipha, sakanalandira nsembe yathu yopsereza+ ndiponso nsembe yathu yambewu. Komanso sakanationetsa ndiponso kutiuza zinthu zonsezi.”
23 Koma mkazi wakeyo anati: “Yehova akanakhala kuti akufuna kutipha, sakanalandira nsembe yathu yopsereza+ ndiponso nsembe yathu yambewu. Komanso sakanationetsa ndiponso kutiuza zinthu zonsezi.”