-
Oweruza 14:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Choncho anakauza bambo ndi mayi ake kuti: “Ndaona mkazi wa Chifilisiti wokongola ku Timuna, ndiye mukanditengere kuti akhale mkazi wanga.”
-