-
Oweruza 14:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma bambo ndi mayi akewo anamʼfunsa kuti: “Kodi sungapeze mkazi pakati pa abale ako kapena pakati pa anthu onse a mtundu wathu?+ Zoona mpaka ukatenge mkazi kwa Afilisiti osadulidwa?” Koma Samisoni anauza bambo akewo kuti: “Ingopitani mukanditengere mkazi ameneyu, chifukwa ndiye woyenera kwa ine.”*
-