Oweruza 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bambo ndi mayi akewo sanadziwe kuti Yehova ndi amene ankachititsa zimenezi chifukwa iye* ankafunafuna mpata woti alange Afilisiti, omwe pa nthawiyi ankalamulira Isiraeli.+
4 Bambo ndi mayi akewo sanadziwe kuti Yehova ndi amene ankachititsa zimenezi chifukwa iye* ankafunafuna mpata woti alange Afilisiti, omwe pa nthawiyi ankalamulira Isiraeli.+