-
Oweruza 14:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho Samisoni anapita ku Timuna pamodzi ndi bambo ndi mayi ake. Atafika mʼminda ya mpesa ya ku Timuna, anakumana ndi mkango ndipo unayamba kubangula.
-