Oweruza 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno mzimu wa Yehova unamupatsa mphamvu,+ moti anakhadzula mkangowo pakati ngati mmene munthu angakhadzulire kamwana ka mbuzi ndi manja. Koma sanauze bambo kapena mayi ake zimene anachitazi. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:6 Nsanja ya Olonda,1/15/2005, tsa. 31
6 Ndiyeno mzimu wa Yehova unamupatsa mphamvu,+ moti anakhadzula mkangowo pakati ngati mmene munthu angakhadzulire kamwana ka mbuzi ndi manja. Koma sanauze bambo kapena mayi ake zimene anachitazi.