Oweruza 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Samisoni anapita kwa mkazi uja nʼkulankhula naye ndipo ankaonabe kuti mkaziyo anali woyenera.+