-
Oweruza 14:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma mukalephera kundiuza tanthauzo lake, inuyo mudzandipatsa malaya 30 ndi zovala zina 30.” Atatero iwo anamuuza kuti: “Nena mwambi wakowo timve.”
-