Oweruza 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho iye anati: “Mʼchinthu chodya zinzake munapezeka chakudya,Ndipo mʼchinthu champhamvu munapezeka zotsekemera.”+ Iwo analephera kumasulira mwambiwo kwa masiku atatu.
14 Choncho iye anati: “Mʼchinthu chodya zinzake munapezeka chakudya,Ndipo mʼchinthu champhamvu munapezeka zotsekemera.”+ Iwo analephera kumasulira mwambiwo kwa masiku atatu.