Oweruza 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma mkaziyo anapitiriza kulirira Samisoni mpaka pa tsiku la 7 la phwandolo. Pamapeto pake, pa tsiku la 7, Samisoni anauza mkaziyo tanthauzo lake chifukwa anamuumiriza. Kenako mkaziyo anauuza anthu a mtundu wake tanthauzo la mwambiwo.+
17 Koma mkaziyo anapitiriza kulirira Samisoni mpaka pa tsiku la 7 la phwandolo. Pamapeto pake, pa tsiku la 7, Samisoni anauza mkaziyo tanthauzo lake chifukwa anamuumiriza. Kenako mkaziyo anauuza anthu a mtundu wake tanthauzo la mwambiwo.+