18 Choncho pa tsiku la 7, dzuwa lisanalowe, amuna amumzindawo anamuuza kuti:
“Kodi chotsekemera kuposa uchi nʼchiyani,
Nanga champhamvu kuposa mkango nʼchiyani?”+
Iye anawayankha kuti:
“Mukanapanda kulima ndi ngʼombe yanga yaikazi,+
Simukanatha kumasulira mwambi wanga.”