-
Oweruza 15:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kenako, pa nthawi yokolola tirigu, Samisoni anapita kukaona mkazi wake uja ndipo anatenga kamwana ka mbuzi. Atafika anati: “Ndikufuna ndilowe kuchipinda kwa mkazi wanga.” Koma bambo a mkaziyo anamukaniza kulowa.
-