-
Oweruza 15:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako anayatsa miyuniyo ndi moto, nʼkukusira nkhandwezo mʼminda ya Afilisti ya mbewu zosakolola. Choncho anayatsa chilichonse, kuyambira mitolo ya mbewu, mbewu zosakolola, minda ya mpesa komanso minda ya maolivi.
-