Oweruza 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atafika naye ku Lehi, Afilisiti nʼkumuona, anafuula chifukwa chosangalala. Ndiyeno mzimu wa Yehova unamupatsa mphamvu,+ ndipo zingwe zimene anamʼmanga nazo manja zija zinadukaduka ngati ulusi wowauka ndi moto nʼkugwa pansi.+
14 Atafika naye ku Lehi, Afilisiti nʼkumuona, anafuula chifukwa chosangalala. Ndiyeno mzimu wa Yehova unamupatsa mphamvu,+ ndipo zingwe zimene anamʼmanga nazo manja zija zinadukaduka ngati ulusi wowauka ndi moto nʼkugwa pansi.+