-
Oweruza 15:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiyeno anamva ludzu koopsa, ndipo anafuulira Yehova kuti: “Ndinu amene mwandipulumutsa ine mtumiki wanu. Ndiye kodi ndife ndi ludzu, nʼkufera mʼmanja mwa anthu osadulidwa?”
-