-
Oweruza 16:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Anthu a ku Gaza anauzidwa kuti: “Samisoni wabwera kuno.” Choncho anazungulira malowo nʼkumubisalira usiku wonse pageti la mzindawo. Iwo anakhala chete usiku wonse nʼkumaganiza kuti: “Kukangocha timupha.”
-