-
Oweruza 16:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma Samisoni anagonabe mpaka pakati pa usiku. Kenako anadzuka pakati pa usikupo nʼkugwira zitseko za geti la mzindawo pamodzi ndi nsanamira zake ziwiri nʼkuzizula pamodzi ndi chokhomera cha getilo. Atatero anazinyamula pamapewa nʼkupita nazo pamwamba pa phiri limene linayangʼanana ndi Heburoni.
-