Oweruza 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Samisoni anamuyankha kuti: “Atandimanga ndi zingwe 7 zatsopano zaziwisi,* ndingafooke nʼkukhala ngati munthu wamba.”
7 Samisoni anamuyankha kuti: “Atandimanga ndi zingwe 7 zatsopano zaziwisi,* ndingafooke nʼkukhala ngati munthu wamba.”